[PDF] Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa - eBooks Review

Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa


Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa
DOWNLOAD

Download Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa PDF/ePub or read online books in Mobi eBooks. Click Download or Read Online button to get Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa book now. This website allows unlimited access to, at the time of writing, more than 1.5 million titles, including hundreds of thousands of titles in various foreign languages. If the content not found or just blank you must refresh this page



Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa


Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa
DOWNLOAD
Author : Dag Heward-Mills
language : ny
Publisher: Parchment House
Release Date : 2015

Zomwe Zikutanthauza Kukhala M Busa written by Dag Heward-Mills and has been published by Parchment House this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Religion categories.


Chinthu chimodzi chokha chimadza kwa inu mukamva mawu akuti "M’busa" - nkhosa! Nkhosa ndi nyama zodalira zome zimafunikira abusa. M’busa ndi wotsogolera wosamalira komanso wachikondi kwa nkhosa. M'Baibulo, Mulungu amatitchula ife ngati gulu la nkhosa za Mulungu. Yesu adamuuza wophunzira Petro kuti adyetse nkhosa zake kuti atsimikizire za chikondi chake cha Mpulumutsi. Kukhala m'busa ndi ntchito yabwino kwambiri. Ndi chinthu chapamwamba kuitanidwa ndi Mulungu ndi kulembetsedwa mwa antchito Ake ndi kusamalira nkhosa. Mu bukhuli, Dag Heward-Mills akutiitanira ife, akutilimbikitsa ndi kutiwonetsa ife momwe tingatengerepo nawo mbali pa ntchito yayikulu yosamalira anthu a Mulungu. Musati muzisiyidwe kunja kwa ntchito yabwino iyi yokhala m’busa!



Zomwe Zikutanthauza Kukhala Wa Nzeru Monga Njoka


Zomwe Zikutanthauza Kukhala Wa Nzeru Monga Njoka
DOWNLOAD
Author : D. A. G. Heward-mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2015

Zomwe Zikutanthauza Kukhala Wa Nzeru Monga Njoka written by D. A. G. Heward-mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Religion categories.


Yesu anati: mukhale ochenjera ngati njoka ndi oona mtima ngati nkhunda. Kodi njoka ndizochenjeradi? Nchifukwa chiyani Yesu angapereke langizo ngati limeneli? Tengani kaulendo mu bukhu lopangitsa chidwiri la Dag Heward-Mills, ndi kuzipezera nzeru zobisika za njoka.



Mpingo Waukulu


Mpingo Waukulu
DOWNLOAD
Author : D. A. G. Heward-mills
language : en
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2015

Mpingo Waukulu written by D. A. G. Heward-mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Religion categories.


“…Tuluka, nupite kumiseu ndi njira za kuminda, nuwaumirize anthu alowe. KUTI NYUMBA YANGA IDZALE.” Luka 14:23. Kulira kwa Mulungu ndi kwakuti dziko lonse lipulumutsidwe, ndi kuti nyumba Yake-tchalitchi-lidzale! Kuchokera ku vumbulutso limeneri bukhu iri linabwera., “Mpingo Waukulu” lolembedwa ndi Bishop Dag Heward-Mills, m’busa wa umodzi mwa mipingo yaikulu kwambiri ku Ghana. Mpingo wanu ndi utumiki wanu sudzakhalanso chimodzi modzi mukawerenga bukhu lolimbikitsali!“Dr. Heward-Mills ndi wodzipereka kwa Ambuye Yesu Khristu ndi ntchito yotenga mbali pa kulalikira ku dziko lonse. Ndi mtsogoleri wamphamvu ndinso chitsanzo ku mautumiki onse, ndipo ife ku “Church Growth International”, ndife olemekezedwa kudziwa ndikumutcha Dr. Dag Heward-Mills mnzathu komanso wogwira naye limodzi ntchito mu kholola lalikulu mu minda ya padziko.” -Dr. Yonggi Cho Wamkulu, Church Growth International



Luso La Ubusa


Luso La Ubusa
DOWNLOAD
Author : D. A. G. Heard-mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2015

Luso La Ubusa written by D. A. G. Heard-mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Young Adult Nonfiction categories.


Ngati ndinu m’busa wa nkhosa za Mulungu, muzathandizika kwambiri ndi ntchito yabwinoyi. Masamba amenewa ali ndi malangizo ofotokozedwa bwino, ofunikira pa kuchita bwino kwanu. Bishop Dag Heward-Mills akutenga kuchokera mukukhala kwake kwa zaka zoposera makumi atatu ngati m’busa, kugawana nafe zinthu zochita mu ntchio ya utumiki. Ngati mwasirira kukhala m’busa wa anthu a Mulungu, iri ndi bukhu lokutsogolerani lomwe mwakhala mukulifuna.



Mwa Inu Mmodzi Ali Mdierekezi


Mwa Inu Mmodzi Ali Mdierekezi
DOWNLOAD
Author : Da Heward-Mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2019-03-21

Mwa Inu Mmodzi Ali Mdierekezi written by Da Heward-Mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2019-03-21 with Religion categories.


Mau opatsa chidwi amenewa “mwa inu mmodzi ndi mdierekezi" analankhulidwa ndi Yesu Khristu pa gulu lake laling’ono la ophunzira khumi ndi awiri. Ambiri a ife timachitiridwa zowawa ndi mdierekezi chifukwa sitimadziwa momwe tingamuonetsera poyera kapenanso kukazindikira zintchito zake. Mu bukhu lodalitsika limeneli, mudzatulukira uchimo wa mdierekezi ndi kupanga chisankho cha kusayenda mmenemo. Zikhale kuti mau awa “mwa inu mmodzi ndi mdierekezi” asakhale akunenera pa inu!



Iwo Amene Ali Odzikuza


Iwo Amene Ali Odzikuza
DOWNLOAD
Author : D. A. G. Heward-mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2015

Iwo Amene Ali Odzikuza written by D. A. G. Heward-mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Young Adult Nonfiction categories.


Kudzikweza ndi poizoni wakupha amene waononga mtundu wa anthu mzaka zambiri. Chifukwa nkosatheka, kudzikweza kumakwaniritsa kupangitsa chionongeko chachikulu popanda kuonekera. Tingamenyane bwanji ndi chiopsezo chimenechi ku miyoyo yathu? Ndi katemera wa kudzichepetsa! Kudzichepetsa ndi chabwino chauzimu. Ochepa akwanitsa kulemba zokhudzana ndi chofunikira chauzimuchi. Mu bukhu latsopano losangalatsali, Dag Heward-Mills akuonetsera mitundi yobisika ya kudzikweza. Bukhu la mphamvu limeneri, lolembedwa ndi Mkhristu wovutika mzathu, likudalitsani ndi kukulimbikitsani inu kukuza kudzichepetsa konga mwana kwa Yesu Khristu.



Luso La Kumva


Luso La Kumva
DOWNLOAD
Author : D. A. G. Heward-mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2015

Luso La Kumva written by D. A. G. Heward-mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Religion categories.


Palibe mutu wofunikira kwambiri kuposa kukhala mu chifuniro cha Mulungu. Chokhacho chomwe chikasiyanitse azitumiki a uthenga ndi kuthekera kwawo kwa kumva mawu a Mulungu molondola. Momwe kulili kwabwino kutsatira Mzimu Woyera ku chifuniro cha Mulungu. Mukakhala mu chifuniro cha Mulungu, muzachita bwino ndipo muzakwaniritsa zokhumba zonse kwa Mulungu. Ntchito yapamwambayi yolembedwa ndi Dag Heward-Mills izakhala ndi kukhudza kwakukulu pa moyo wanu ndi utumiki.



Zolakwika Khumi Zoyambilira Zimene Abusa Amachita


Zolakwika Khumi Zoyambilira Zimene Abusa Amachita
DOWNLOAD
Author : Dag Heward-Mills
language : ny
Publisher: Parchment House
Release Date : 2015

Zolakwika Khumi Zoyambilira Zimene Abusa Amachita written by Dag Heward-Mills and has been published by Parchment House this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Religion categories.


Baibulo limatiuza kuti tonse timalakwitsa- Abusa nawo amalakwitsanso. Kulakwitsa kumabwezeretsa m’mbuyo. Kulakwitsa kumalepheretsa kupita chitsogolo. Kodi ndi zolakwitsa ziti zimene abusa anu apanga? Kodi ndi chiyani chingakhale zolakwitsa zazikulu khumi zimene abusa amachita? Muli omasuka kuwerenga Bukuli ndi kuzindikira zolakwika zimene mungazichite ndi m'mene mungazipewere. Buku lofunikali lidzakhala mdalitso kwa inu ndi utumiki wanu.



Kukula Kwa Mpingo


Kukula Kwa Mpingo
DOWNLOAD
Author : D. A. G. Heward-mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2015

Kukula Kwa Mpingo written by D. A. G. Heward-mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2015 with Architecture categories.


Tikudziwa kui kukula kwa mpingo ndi chinthu chovuta kukwaniritsa. azibusa onse amafuna mpingo wawo ukule. bukhuli ndi yankho la kufuna kwanu kwa kukula kwa mpingo. mukamvetsetsa momwe "zinthu zosiyanasiyana zimawirira pamodzi" kukwaniritsa kukula kwa mpingo. wokondedwa m'busa, pomwe mawu ndi kudzoza kuli m'bukhuli kukubwera mu mtima mwanu, muzakhala ndi kukula kwa mpingo komwe mwakhala mukupempherera



Luso La Utumiki


Luso La Utumiki
DOWNLOAD
Author : Dag Heward-Mills
language : ny
Publisher: Dag Heward-Mills
Release Date : 2019-04-11

Luso La Utumiki written by Dag Heward-Mills and has been published by Dag Heward-Mills this book supported file pdf, txt, epub, kindle and other format this book has been release on 2019-04-11 with Religion categories.


Kukuza luso ndiko kukuza kuthekera. Baibulo limanena kuti kukonderedwa kumadza kwa anthu a luso. Ntchito ya utumiki imafuna kuthekera kwa kukulu. Bukhu latsopanoli, “Luso la Utumiki” ndi lofunika kwambiri kwa onse amene amakhumbira kuchita ntchito ya Mulungu. Limawonetseratu maganizo omwe ali olondola ndi oipa okhudzana ndi utumiki, chomwe ntchito ya utumiki chiri, chomwe mukuyenera kuchita ngati wogwira ntchito mu utumiki ndi momwe mungapangire ntchito za mtumiki. Mwadabwapo zokhuzana ndi momwe mungachitire ntchito ya utumiki? Bukhu lapaderali lolembedwa ndi Dag Heward-Mills likakulimbikitsani inu kuyenda moyenereza maitanidwe an a Mulungu ndi kukutsogozani inu mu kudzipereka nokha kwathunthu ku ntchito ya Mulungu.